• Tidak ada hasil yang ditemukan

smallholder tea poster12sep

N/A
N/A
Protected

Academic year: 2017

Membagikan "smallholder tea poster12sep"

Copied!
1
0
0

Teks penuh

(1)

Ndondomeko zofunikira za ulimi oyenera

Version: June 2011

Kuteteza mbewu ku tizilombo (kuthana ndi matenda

wotchedwa Armilaria owononga mitengo ya tiyi)

Kasamalidwe ka zinyalala za pulasitiki ndi mabotolo

a mankhwala

Kusamala chilengedwe

Kuteteza mbewu ku tizilombo (kutengulira)

Zipangizo zozitetezela

Kasungidwe ka mankhwala

Kasamalidwe ka zinyalala zomwe zimatha kuwola

Kuteteza nthaka kuti

isakokoloke

Kusamala madzi oyipa pakhomo

Mabotolo opanda kanthu komanso zinyalala za pulasitiki zatayidwa pansi

Mwachitsanzo, khola lankhuku lakale mutha kulisandutsa mosungira mankhwala. Ikanimo pulasitiki mkati

Kusunga mankhwala m'nyumba

Za alimi ang'onoang'ono a tiyi

-Mtengo wa tiyi wang'aluka ndipo ukutulutsa tiufa toyera

Zulani phata lonse ndi mizu yomwe ndipo mutenthe

Kutengulira tiyi kuti tizilombo tisapitilire kufala. Nthambi zomwe zadulidwa zitha kugwiritsidwa ntchito pophimbira mbewu.

Tizilombo tikupitilira kuwononga tiyi

Kupopela osaziteteza

Chovala kunkhope chotchinjiliza

kuti mankhwala asakukhudzeni Chovala choteteza ku mvula

M'golo wa chitsulo mutha kuusandutsa mosungira

Potolela mabotolo a mankhwala ndi zinyalala za pulasitiki, onetsetsani kuti mwazisiyanitsa (pamapeto pa zonse, otsogolera gulu watolela zonse)

Kuwotcha zinyalala Kupanga manyowa kuchokela ku zinyalala zomwe zimatha kuwola

Kutaya madzi oyipa kutsogolo kwa nyumba

Kutaya madzi mu nkhuti momwe mwabzalidwa nthochi (Dziwani izi: ngati madzi akupanga zithaphwi (sakuyenda), mukumbe dzenje ndikuikamo miyala)

Kuzula bulugama amene ali pafupi ndi mtsinje

Mtsinje wabwelera mchimake Bulugama amaumitsa

mitsinje ndi zitsime

Vuto la kukokoloka kwa nthaka

Kubzala mitengo yachilengedwe ndi nsenjere kuti muteteze nthaka komanso madzi

Mabotolo opanda

zinyalala za pulasitiki

Kutsuka zipangizo

Kutsuka zipangizo mu mtsinje kapena dziwe

Kutaya madzi ochapila mu dimba lomwe lathilidwa mankhwala

Kapena, kutaya madzi mu nkhuti yomwe muli makala

Bulugama

Mtsinje ukuwuma

Madzi

Referensi

Dokumen terkait

Pertanyaan yang sama dilakukan kepada anak didik setelah mengi- kuti serangkaian pembelajaran tematik kelautan menghasilkan jawaban yang sedikit mengalami perubahan,

Jalan Sultan Mahmud Badarudin II No.2 Telp (0733) 451243. Fax 451233 Kel Air Kuti Lubuk Linggau

Penelitian ini akan dilaksanakan di STKIP-PGRI Lubuklinggau Jalan Mayor Toha Kelurahan Air Kuti Kecamatan Lubuklinggau Timut I Kota Lubuklinggau. Populasi dalam

keterbatasannya (Candra, 2010). Bagaimana petani perkebunan rakyat menghadapi sistem sertifikasi merupakan isu yang sangat menarik untuk dikaji. Penelitian ini bertujuan

 Prevent erosion by letting natural vegetation grow or by planting and grasses and trees on river

Penyebab siswa yang mengi- kuti pembelajaran TSTS mempunyai peningkatan kemampuan representasi matematis lebih tinggi daripada siswa yang mengikuti pembelajaran diskusi

Pemberontakan di Majapahit Pemberontakan Ranggalawe Pemberontakan Lembu Sora Pemberontakan Nambi Pemberontakan Kuti Pemberontakan Tanca Pemberontakan Sadeng-Keta Masa Kejayaan Kerajaan

Dalam memastikan semua karyawan Laundry memberikan layanan yang professional, usaha Supervisor untuk karyawan Laundry adalah membuat karyawan menjadi kompak dalam bekerja, adapun